Yohane 6:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pambuyo pa zimenezi, Yesu anawolokera kutsidya lina la nyanja ya Galileya,* kapena kuti nyanja ya Tiberiyo.+ 2 Ndipo gulu lalikulu la anthu linkamutsatira+ chifukwa linkaona zizindikiro zimene iye ankachita pochiritsa anthu odwala.+
6 Pambuyo pa zimenezi, Yesu anawolokera kutsidya lina la nyanja ya Galileya,* kapena kuti nyanja ya Tiberiyo.+ 2 Ndipo gulu lalikulu la anthu linkamutsatira+ chifukwa linkaona zizindikiro zimene iye ankachita pochiritsa anthu odwala.+