Mateyu 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yesu atamva zimenezi, anachoka kumeneko pangalawa nʼkupita kumalo kopanda anthu kuti akakhale payekha. Koma gulu la anthu litamva zimenezo, linamutsatira wapansi kuchokera mʼmizinda yawo.+ Luka 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atumwi aja atabwerako anafotokozera Yesu zimene anachita.+ Atatero anawatenga nʼkupita nawo kwaokha mumzinda wotchedwa Betsaida.+
13 Yesu atamva zimenezi, anachoka kumeneko pangalawa nʼkupita kumalo kopanda anthu kuti akakhale payekha. Koma gulu la anthu litamva zimenezo, linamutsatira wapansi kuchokera mʼmizinda yawo.+
10 Atumwi aja atabwerako anafotokozera Yesu zimene anachita.+ Atatero anawatenga nʼkupita nawo kwaokha mumzinda wotchedwa Betsaida.+