Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma iwe ukamapemphera, uzilowa mʼchipinda chako nʼkutseka chitseko ndipo uzipemphera kwa Atate wako amene sungathe kuwaona.+ Ukatero Atate wako amene akuona zimene zikuchitika ngakhale kuti iweyo sungathe kuwaona, adzakubwezera.

  • Mateyu 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Atauza anthuwo kuti azipita, anakwera phiri yekhayekha kukapemphera.+ Iye anakhala kumeneko yekhayekha mpaka kunja kunada.

  • Maliko 1:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mʼmawa kwambiri kudakali mdima, Yesu anadzuka nʼkutuluka panja ndipo anapita kumalo kopanda anthu. Kumeneko anayamba kupemphera.+

  • Luka 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mʼmasiku amenewo, Yesu anapita kuphiri kukapemphera+ ndipo anachezera usiku wonse kupemphera kwa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena