Mateyu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzamva phokoso la nkhondo ndi malipoti a nkhondo. Izitu zisadzakuchititseni mantha, chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+ Luka 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso, mukadzamva phokoso la nkhondo ndi zipolowe,* musadzachite mantha. Chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika choyamba, koma mapeto sadzafika nthawi yomweyo.”+
6 Mudzamva phokoso la nkhondo ndi malipoti a nkhondo. Izitu zisadzakuchititseni mantha, chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+
9 Komanso, mukadzamva phokoso la nkhondo ndi zipolowe,* musadzachite mantha. Chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika choyamba, koma mapeto sadzafika nthawi yomweyo.”+