Mateyu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzamva phokoso la nkhondo ndi malipoti a nkhondo. Izitu zisadzakuchititseni mantha, chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+ Maliko 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso mukadzamva phokoso la nkhondo ndi malipoti a nkhondo, musadzachite mantha. Zimenezi zikuyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+
6 Mudzamva phokoso la nkhondo ndi malipoti a nkhondo. Izitu zisadzakuchititseni mantha, chifukwa zimenezi zikuyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+
7 Komanso mukadzamva phokoso la nkhondo ndi malipoti a nkhondo, musadzachite mantha. Zimenezi zikuyenera kuchitika ndithu, koma mapeto adzakhala asanafikebe.+