Ekisodo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Mose anatenga magaziwo nʼkuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndi magazi a pangano limene Yehova wapangana nanu mogwirizana ndi mawu onsewa.”+ Levitiko 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa moyo wa nyama uli mʼmagazi+ ndipo ine ndawapereka paguwa lansembe+ kuti azikuphimbirani machimo. Zili choncho chifukwa magazi ndi amene amaphimba machimo+ chifukwa cha moyo umene uli mʼmagaziwo. Aheberi 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mogwirizana ndi Chilamulo, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ ndipo popanda kukhetsa magazi anthu sangakhululukidwe machimo awo.+
8 Choncho Mose anatenga magaziwo nʼkuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndi magazi a pangano limene Yehova wapangana nanu mogwirizana ndi mawu onsewa.”+
11 Chifukwa moyo wa nyama uli mʼmagazi+ ndipo ine ndawapereka paguwa lansembe+ kuti azikuphimbirani machimo. Zili choncho chifukwa magazi ndi amene amaphimba machimo+ chifukwa cha moyo umene uli mʼmagaziwo.
22 Mogwirizana ndi Chilamulo, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ ndipo popanda kukhetsa magazi anthu sangakhululukidwe machimo awo.+