Yohane 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano dziko ili likuweruzidwa, wolamulira wa dzikoli+ aponyedwa kunja tsopano.+ Yohane 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Sindilankhula nanu zambiri chifukwa wolamulira wa dziko+ akubwera ndipo alibe mphamvu pa ine.+ Aefeso 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawi ina munkachita zimenezi mogwirizana ndi nthawi* za mʼdzikoli,+ pomvera wolamulira wa mpweya+ umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe+ kameneka, tsopano kakugwira ntchito mwa ana osamvera.
2 Pa nthawi ina munkachita zimenezi mogwirizana ndi nthawi* za mʼdzikoli,+ pomvera wolamulira wa mpweya+ umene umalamulira zochita za anthu. Mpweya umenewu, kapena kuti kaganizidwe+ kameneka, tsopano kakugwira ntchito mwa ana osamvera.