Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako ndinamva mawu a munthu kuchokera pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anaitana kuti: “Gabirieli,+ munthuyo umuthandize kuti amvetsetse zimene waona.”+

  • Danieli 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 inde, ndili mkati molankhula zimenezi mʼpemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona mʼmasomphenya poyamba paja,+ anabwera kwa ine nditatopa kwambiri, pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo imene imaperekedwa ngati mphatso.

  • Luka 1:26, 27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Elizabeti ali woyembekezera kwa miyezi 6, Mulungu anatumiza mngelo Gabirieli+ kumzinda wina wa ku Galileya, wotchedwa Nazareti. 27 Anamutumiza kwa namwali+ amene mwamuna wina dzina lake Yosefe, wa mʼnyumba ya Davide, anamulonjeza* kuti adzamukwatira. Namwali ameneyu dzina lake anali Mariya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena