Mateyu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iye anawayankha kuti: “Mutakhala ndi nkhosa imodzi yokha, ndiyeno nkhosayo nʼkugwera mʼdzenje pa tsiku la Sabata, kodi alipo pakati panu amene sangaigwire nʼkuitulutsa?+ Maliko 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiyani pa Sabata, chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete. Yohane 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ngati munthu amadulidwa tsiku la sabata posafuna kuphwanya Chilamulo cha Mose, kodi mukundipsera mtima kwambiri chifukwa ndinachiritsa munthu tsiku la sabata?+
11 Koma iye anawayankha kuti: “Mutakhala ndi nkhosa imodzi yokha, ndiyeno nkhosayo nʼkugwera mʼdzenje pa tsiku la Sabata, kodi alipo pakati panu amene sangaigwire nʼkuitulutsa?+
4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiyani pa Sabata, chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete.
23 Ngati munthu amadulidwa tsiku la sabata posafuna kuphwanya Chilamulo cha Mose, kodi mukundipsera mtima kwambiri chifukwa ndinachiritsa munthu tsiku la sabata?+