Maliko 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Nsanja ya Olonda,10/15/1997, tsa. 30
4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete.