Luka 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zogwera pathanthwe ndi anthu amene amati akangomva mawuwo, amawalandira mosangalala, koma oterewa alibe mizu. Amakhulupirira kwa kanthawi, koma nthawi yoyesedwa ikafika amagwa.+
13 Zogwera pathanthwe ndi anthu amene amati akangomva mawuwo, amawalandira mosangalala, koma oterewa alibe mizu. Amakhulupirira kwa kanthawi, koma nthawi yoyesedwa ikafika amagwa.+