-
Mateyu 13:34, 35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Yesu analankhula zonsezi ndi gulu la anthulo pogwiritsa ntchito mafanizo. Ndithudi, nthawi zonse iye ankalankhula nawo pogwiritsa ntchito mafanizo,+ 35 kuti zimene Mulungu ananena kudzera mwa mneneri zikwaniritsidwe. Mneneriyo anati: “Ndidzatsegula pakamwa panga nʼkunena mafanizo. Ndidzafalitsa zinthu zimene zinabisika kuchokera pachiyambi.”*+
-