Mateyu 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ndithu ndikukuuzani, zidzakhala zovuta kuti munthu wolemera adzalowe mu Ufumu wakumwamba.+ 1 Timoteyo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma anthu ofunitsitsa kulemera amakumana ndi mayesero ndiponso amakodwa mumsampha.+ Iwo amalakalaka zinthu zowapweteketsa komanso amachita zinthu mopanda nzeru. Zimenezi zimawawononga ndiponso kuwabweretsera mavuto.+
23 Ndiyeno Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ndithu ndikukuuzani, zidzakhala zovuta kuti munthu wolemera adzalowe mu Ufumu wakumwamba.+
9 Koma anthu ofunitsitsa kulemera amakumana ndi mayesero ndiponso amakodwa mumsampha.+ Iwo amalakalaka zinthu zowapweteketsa komanso amachita zinthu mopanda nzeru. Zimenezi zimawawononga ndiponso kuwabweretsera mavuto.+