Mateyu 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Imene inafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa mʼnthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula ndipo sabereka zipatso.+
22 Imene inafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa mʼnthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula ndipo sabereka zipatso.+