Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 6:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chifukwa kumene kuli chuma chako, mtima wako udzakhalanso komweko.

  • Maliko 4:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiye palinso mbewu zina zimene zimafesedwa paminga. Amenewa ndi anthu amene amamva mawu,+ 19 koma nkhawa za moyo+ wamʼnthawi* ino, chinyengo champhamvu cha chuma+ komanso kulakalaka zinthu+ zina zonse, zimalowa mʼmitima yawo nʼkulepheretsa mawuwo kukula ndipo sabereka zipatso.

  • Maliko 10:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yesu atayangʼana uku ndi uku, anauza ophunzira akewo kuti: “Zidzakhalatu zovuta kwambiri kuti anthu andalama adzalowe mu Ufumu wa Mulungu!”+

  • Luka 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Zimene zinagwera paminga, ndi anthu amene amva mawu a Mulungu koma chifukwa chotengeka ndi nkhawa, chuma+ ndi zosangalatsa za moyo uno,+ amalephera kukula bwino ndipo zipatso zawo sizikhwima.+

  • 1 Timoteyo 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma anthu ofunitsitsa kulemera amakumana ndi mayesero ndiponso amakodwa mumsampha.+ Iwo amalakalaka zinthu zowapweteketsa komanso amachita zinthu mopanda nzeru. Zimenezi zimawawononga ndiponso kuwabweretsera mavuto.+

  • 2 Timoteyo 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kuno Dema+ wandisiya chifukwa chokonda zinthu zamʼdzikoli* ndipo wapita ku Tesalonika. Keresike wapita ku Galatiya ndipo Tito wapita ku Dalimatiya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena