Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 14:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pamenepo amene anali mʼngalawamo anamugwadira nʼkunena kuti: “Ndinudi Mwana wa Mulungu.”

  • Yohane 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Yohane anachitiranso umboni kuti: “Ndinaona mzimu ukutsika ngati nkhunda kuchokera kumwamba ndipo unakhalabe pa iye.+

  • Yohane 1:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ine ndinaonadi zimenezo ndipo ndachitira umboni kuti iyeyu ndi Mwana wa Mulungu.”+

  • Yohane 20:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Koma izi zalembedwa kuti mukhulupirire kuti Yesu ndi Khristu, Mwana wa Mulungu, komanso chifukwa choti mwakhulupirira, mukhale ndi moyo mʼdzina lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena