Luka 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako anati: “Mwana wa munthu akuyenera kukumana ndi mavuto ambiri ndiponso kukanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndipo adzaphedwa+ nʼkuukitsidwa patapita masiku atatu.”+ Luka 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Komabe ndiyenera kupitiriza ulendo wanga lero ndi mawa ndi tsiku linalo, chifukwa nʼkosayenera kuti mneneri amuphere kunja kwa Yerusalemu.+
22 Kenako anati: “Mwana wa munthu akuyenera kukumana ndi mavuto ambiri ndiponso kukanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndipo adzaphedwa+ nʼkuukitsidwa patapita masiku atatu.”+
33 Komabe ndiyenera kupitiriza ulendo wanga lero ndi mawa ndi tsiku linalo, chifukwa nʼkosayenera kuti mneneri amuphere kunja kwa Yerusalemu.+