Yesaya 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Analandira chilango kuti ife tikhale pamtendere,+Ndipo chifukwa cha mabala ake ifeyo tinachiritsidwa.+ Yesaya 53:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.Ndi ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mʼbadwo wa makolo ake?* Popeza iye anadulidwa mʼdziko la anthu amoyo.+Iye anakwapulidwa* chifukwa cha zolakwa za anthu anga.+ Luka 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma choyamba akuyenera kukumana ndi mavuto ambiri komanso kukanidwa ndi mʼbadwo uwu.+
5 Koma iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Analandira chilango kuti ife tikhale pamtendere,+Ndipo chifukwa cha mabala ake ifeyo tinachiritsidwa.+
8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.Ndi ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mʼbadwo wa makolo ake?* Popeza iye anadulidwa mʼdziko la anthu amoyo.+Iye anakwapulidwa* chifukwa cha zolakwa za anthu anga.+