Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 “Iwe lupanga, nyamuka ubaye mʼbusa wanga.+

      Ubaye munthu yemwe ndi mnzanga,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

      “Ipha mʼbusa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+

      Ine ndidzalanga nkhosa zonyozeka.”

  • Yohane 11:49, 50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Koma mmodzi wa iwo, Kayafa,+ amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho, anati: “Palibe chimene mukudziwa inu 50 ndipo simukuona kuti nʼzothandiza kwa inu kuti munthu mmodzi afere anthu onse mʼmalo moti mtundu wonse uwonongeke.”

  • Aroma 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamene tinalibe mtengo wogwira,*+ Khristu anafera anthu osalambira Mulungu pa nthawi imene anakonzeratu.

  • Aheberi 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Zikanatero, akanavutika mobwerezabwereza kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa. Koma tsopano iye waonekera kamodzi kokha pamapeto a nthawi* ino kuti achotse uchimo kudzera mu nsembe yake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena