Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pali milungu* 70 imene yaikidwa yokhudza anthu a mtundu wako ndi mzinda wanu woyera+ ndi cholinga choti athetse kuphwanya malamulo, athetse machimo,+ aphimbe cholakwa,+ abweretse chilungamo kuti chikhalepo mpaka kalekale,+ adinde chidindo pamasomphenya ndi maulosi,*+ ndiponso kuti adzoze Malo Opatulika Koposa.*

  • Aheberi 7:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mosiyana ndi akulu a ansembe ena, iye safunikira kupereka tsiku ndi tsiku nsembe+ za machimo ake choyamba, kenako za anthu ena.+ Zili choncho chifukwa iye anadzipereka kamodzi kokha kuti akhale nsembe yothandiza anthu mpaka kalekale.+

  • 1 Petulo 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pajatu ngakhale Khristu anafa kamodzi kokha kuti achotse uchimo.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama+ kuti akugwirizanitseni ndi Mulungu.+ Iye anaphedwa monga munthu,*+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena