Maliko 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Komanso anayamba kuwaphunzitsa kuti Mwana wa munthu akuyenera kukumana ndi mavuto ambiri ndiponso kukanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndipo adzaphedwa+ nʼkuukitsidwa patapita masiku atatu.+ Maliko 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa iye ankaphunzitsa ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa mʼmanja mwa anthu ndipo adzamupha.+ Koma ngakhale adzamuphe, adzauka patatha masiku atatu.”+ Luka 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako anati: “Mwana wa munthu akuyenera kukumana ndi mavuto ambiri ndiponso kukanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndipo adzaphedwa+ nʼkuukitsidwa patapita masiku atatu.”+
31 Komanso anayamba kuwaphunzitsa kuti Mwana wa munthu akuyenera kukumana ndi mavuto ambiri ndiponso kukanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndipo adzaphedwa+ nʼkuukitsidwa patapita masiku atatu.+
31 Chifukwa iye ankaphunzitsa ophunzira ake nʼkuwauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa mʼmanja mwa anthu ndipo adzamupha.+ Koma ngakhale adzamuphe, adzauka patatha masiku atatu.”+
22 Kenako anati: “Mwana wa munthu akuyenera kukumana ndi mavuto ambiri ndiponso kukanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndipo adzaphedwa+ nʼkuukitsidwa patapita masiku atatu.”+