Luka 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ali mkati molankhula zimenezi, mayi wina mʼgulu la anthulo anafuula nʼkumuuza kuti: “Wosangalala ndi mayi amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!”+
27 Ali mkati molankhula zimenezi, mayi wina mʼgulu la anthulo anafuula nʼkumuuza kuti: “Wosangalala ndi mayi amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!”+