Salimo 71:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Mwachita zinthu zazikulu,Inu Mulungu, ndi ndani angafanane nanu?+ Salimo 111:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wawombola anthu ake.+ צ [Tsade] Walamula kuti pangano lake likhalepo mpaka kalekale. ק [Qoph] Dzina lake ndi loyera komanso lochititsa mantha.+
19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Mwachita zinthu zazikulu,Inu Mulungu, ndi ndani angafanane nanu?+
9 Wawombola anthu ake.+ צ [Tsade] Walamula kuti pangano lake likhalepo mpaka kalekale. ק [Qoph] Dzina lake ndi loyera komanso lochititsa mantha.+