Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 22:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Musamadetse dzina langa loyera,+ mʼmalomwake muzindiona kuti ndine wopatulika pakati pa Aisiraeli.+ Ine ndine Yehova amene ndikukuyeretsani.+

  • Yesaya 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzakwezeka chifukwa cha chiweruzo chake.*

      Mulungu woona, Woyera,+ adzadziyeretsa kudzera mʼchilungamo.+

  • Ezekieli 36:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 ‘Ndidzayeretsadi dzina langa lalikulu+ limene linadetsedwa pakati pa anthu a mitundu ina. Inu munadetsa dzina langalo pakati pa anthu a mitundu ina. Anthu a mitundu inawo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,+ akadzaona zimene ndakuchitirani komanso adzadziwa kuti ndine Mulungu woyera,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena