Genesis 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ili ndi pangano la pakati pa ine ndi iwe, lakuti iwe ndi mbadwa zako muzilisunga: Mwamuna aliyense pakati panu azidulidwa.+ Genesis 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ mʼmibadwo yanu yonse. Aliyense amene wabadwira mʼnyumba yanu komanso aliyense amene si mbadwa yanu koma munamugula ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa. Levitiko 12:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mkazi akakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira pa nthawi imene akusamba.+ 3 Pa tsiku la 8, mwanayo azidulidwa.+
10 Ili ndi pangano la pakati pa ine ndi iwe, lakuti iwe ndi mbadwa zako muzilisunga: Mwamuna aliyense pakati panu azidulidwa.+
12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ mʼmibadwo yanu yonse. Aliyense amene wabadwira mʼnyumba yanu komanso aliyense amene si mbadwa yanu koma munamugula ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa.
2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mkazi akakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira pa nthawi imene akusamba.+ 3 Pa tsiku la 8, mwanayo azidulidwa.+