Mateyu 6:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Musamadere nkhawa za mawa,+ chifukwa mawalo lidzakhala ndi zodetsa nkhawa zakenso. Mavuto a tsiku lililonse ndi okwanira pa tsikulo.”
34 Musamadere nkhawa za mawa,+ chifukwa mawalo lidzakhala ndi zodetsa nkhawa zakenso. Mavuto a tsiku lililonse ndi okwanira pa tsikulo.”