Miyambo 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kudzikuza kwa munthu kudzamutsitsa,+Koma amene ali ndi mtima wodzichepetsa adzapeza ulemerero.+ Mateyu 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aliyense amene amadzikweza adzatsitsidwa,+ koma aliyense amene amadzichepetsa adzakwezedwa.+ Luka 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndithu ndikukuuzani, munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kuti ndi wolungama kwambiri kuposa Mfarisi uja.+ Chifukwa aliyense wodzikweza adzachititsidwa manyazi, koma aliyense amene amadzichepetsa adzakwezedwa.”+ Yakobo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+
14 Ndithu ndikukuuzani, munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kuti ndi wolungama kwambiri kuposa Mfarisi uja.+ Chifukwa aliyense wodzikweza adzachititsidwa manyazi, koma aliyense amene amadzichepetsa adzakwezedwa.”+
6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+