Machitidwe 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho nyumba yonse ya Isiraeli idziwe ndithu kuti Yesu ameneyu, amene inu munamuphera pamtengo,+ Mulungu anamuika kukhala Ambuye+ ndi Khristu.” Afilipi 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso kuti aliyense avomereze poyera kuti Yesu Khristu ndi Ambuye,+ zimene zidzapereka ulemerero kwa Mulungu Atate.
36 Choncho nyumba yonse ya Isiraeli idziwe ndithu kuti Yesu ameneyu, amene inu munamuphera pamtengo,+ Mulungu anamuika kukhala Ambuye+ ndi Khristu.”
11 Komanso kuti aliyense avomereze poyera kuti Yesu Khristu ndi Ambuye,+ zimene zidzapereka ulemerero kwa Mulungu Atate.