Mateyu 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako chizindikiro cha Mwana wa munthu chidzaonekera kumwamba ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni.+ Iwo adzaona Mwana wa munthu+ akubwera pamitambo ya kumwamba ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+ Maliko 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anthu adzaona Mwana wa munthu+ akubwera mʼmitambo ndi mphamvu yaikulu ndiponso ulemerero.+ Chivumbulutso 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Akubwera ndi mitambo+ ndipo diso lililonse lidzamuona, ngakhalenso anthu amene anamubaya. Ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa pomva chisoni chifukwa cha iye.+ Inde, zimenezi zidzachitikadi. Ame.
30 Kenako chizindikiro cha Mwana wa munthu chidzaonekera kumwamba ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni.+ Iwo adzaona Mwana wa munthu+ akubwera pamitambo ya kumwamba ndi mphamvu ndiponso ulemerero waukulu.+
7 Taonani! Akubwera ndi mitambo+ ndipo diso lililonse lidzamuona, ngakhalenso anthu amene anamubaya. Ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa pomva chisoni chifukwa cha iye.+ Inde, zimenezi zidzachitikadi. Ame.