Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,

      Ndipo anthu olemekezeka asonkhana pamodzi* mogwirizana+

      Kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.*+

  • Mateyu 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mʼmawa kutacha, ansembe aakulu onse limodzi ndi akulu a anthu anakambirana nʼkugwirizana kuti aphe Yesu.+

  • Maliko 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+

  • Machitidwe 4:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mafumu a dziko lapansi anaima pamalo awo, ndipo olamulira anasonkhana mogwirizana kuti alimbane ndi Yehova* komanso wodzozedwa* wake.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena