Yesaya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu amene ankayenda mumdimaAona kuwala kwakukulu. Anthu amene ankakhala mʼdziko lamdima wandiweyani,Kuwala kwawawalira.+ Mateyu 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 anthu amene ankakhala mumdima anaona kuwala kwakukulu, ndipo anthu amene ankakhala mʼdera lamthunzi wa imfa, kuwala+ kunawaunikira.”+
2 Anthu amene ankayenda mumdimaAona kuwala kwakukulu. Anthu amene ankakhala mʼdziko lamdima wandiweyani,Kuwala kwawawalira.+
16 anthu amene ankakhala mumdima anaona kuwala kwakukulu, ndipo anthu amene ankakhala mʼdera lamthunzi wa imfa, kuwala+ kunawaunikira.”+