Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 6:47-51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Kunja kutada, ngalawa ija inali ili pakati pa nyanja, koma iye anali yekha kumtunda.+ 48 Ataona ophunzirawo akupalasa movutika chifukwa cholimbana ndi mphepo yamphamvu, iye anawalondola akuyenda panyanja. Uwu unali mʼbandakucha pafupifupi pa ulonda wa 4.* Koma ophunzirawo ankaona ngati akufuna kuwapitirira. 49 Atamuona akuyenda panyanjapo ophunzirawo anaganiza kuti: “Amenewa ndi masomphenya ndithu!” Ndipo anafuula mokweza. 50 Anachita zimenezi chifukwa onsewo anamuona ndipo anachita mantha. Koma nthawi yomweyo iye anawauza kuti: “Mtima mʼmalo, ndine. Musachite mantha.”+ 51 Ndiyeno Yesu anakwera nawo mʼngalawamo ndipo mphepoyo inaleka. Ataona zimenezi anadabwa kwambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena