Maliko 6:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kenako anaona ophunzirawo akupalasa movutika,+ chifukwa anali kulimbana ndi mphepo yamphamvu. Uwu unali m’bandakucha pafupifupi pa ulonda wachinayi,* ndipo iye anawalondola akuyenda panyanja. Koma ophunzirawo anaona ngati akufuna kuwapitirira. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:48 Yesu—Ndi Njira, tsa. 131 Nsanja ya Olonda,1/1/2000, tsa. 32
48 Kenako anaona ophunzirawo akupalasa movutika,+ chifukwa anali kulimbana ndi mphepo yamphamvu. Uwu unali m’bandakucha pafupifupi pa ulonda wachinayi,* ndipo iye anawalondola akuyenda panyanja. Koma ophunzirawo anaona ngati akufuna kuwapitirira.