Maliko 6:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ataona ophunzirawo akupalasa movutika chifukwa cholimbana ndi mphepo yamphamvu, iye anawalondola akuyenda panyanja. Uwu unali mʼbandakucha pafupifupi pa ulonda wa 4.* Koma ophunzirawo ankaona ngati akufuna kuwapitirira. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:48 Yesu—Ndi Njira, tsa. 131 Nsanja ya Olonda,1/1/2000, tsa. 32
48 Ataona ophunzirawo akupalasa movutika chifukwa cholimbana ndi mphepo yamphamvu, iye anawalondola akuyenda panyanja. Uwu unali mʼbandakucha pafupifupi pa ulonda wa 4.* Koma ophunzirawo ankaona ngati akufuna kuwapitirira.