Yohane 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma amene adzamwe madzi amene ine ndidzamupatse sadzamvanso ludzu ngakhale pangʼono.+ Madzi amene ndidzamupatsewo adzasanduka kasupe wa madzi amene akutuluka mwa iye nʼkumupatsa moyo wosatha.”+ Yohane 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pa tsiku lomaliza, tsiku lalikulu la chikondwererocho,+ Yesu anaimirira nʼkufuula kuti: “Ngati wina akumva ludzu, abwere kwa ine adzamwe madzi.+ Chivumbulutso 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mzimu ndi mkwatibwi+ akupitiriza kunena kuti, “Bwera!” ndipo aliyense amene wamva anene kuti, “Bwera!” Komanso aliyense amene akumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi opatsa moyo kwaulere.+
14 Koma amene adzamwe madzi amene ine ndidzamupatse sadzamvanso ludzu ngakhale pangʼono.+ Madzi amene ndidzamupatsewo adzasanduka kasupe wa madzi amene akutuluka mwa iye nʼkumupatsa moyo wosatha.”+
37 Pa tsiku lomaliza, tsiku lalikulu la chikondwererocho,+ Yesu anaimirira nʼkufuula kuti: “Ngati wina akumva ludzu, abwere kwa ine adzamwe madzi.+
17 Mzimu ndi mkwatibwi+ akupitiriza kunena kuti, “Bwera!” ndipo aliyense amene wamva anene kuti, “Bwera!” Komanso aliyense amene akumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi opatsa moyo kwaulere.+