Deuteronomo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzawapatsa mneneri ngati iwe kuchokera pakati pa abale awo.+ Ndidzaika mawu anga mʼkamwa mwake,+ ndipo adzawauza zonse zimene ndidzamulamule.+ Yohane 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthuwo ataona chizindikiro chimene anachitacho, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri uja amene anati adzabwera padziko.”+
18 Ndidzawapatsa mneneri ngati iwe kuchokera pakati pa abale awo.+ Ndidzaika mawu anga mʼkamwa mwake,+ ndipo adzawauza zonse zimene ndidzamulamule.+
14 Anthuwo ataona chizindikiro chimene anachitacho, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri uja amene anati adzabwera padziko.”+