Mateyu 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine+ ndipo palibe amene akumudziwa bwino Mwana koma Atate okha.+ Komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+ Yohane 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu inu mukanakhala kuti mukundidziwa, mukanadziwanso Atate wanga. Kuyambira panopa muwadziwa ndipotu mwawaona kale.”+
27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine+ ndipo palibe amene akumudziwa bwino Mwana koma Atate okha.+ Komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+
7 Anthu inu mukanakhala kuti mukundidziwa, mukanadziwanso Atate wanga. Kuyambira panopa muwadziwa ndipotu mwawaona kale.”+