Yohane 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepa ankanena za mzimu umene onse amene anamukhulupirira anali atatsala pangʼono kulandira. Pa nthawiyi nʼkuti anthu asanalandire mzimu+ chifukwa Yesu anali asanalandire ulemerero wake.+
39 Pamenepa ankanena za mzimu umene onse amene anamukhulupirira anali atatsala pangʼono kulandira. Pa nthawiyi nʼkuti anthu asanalandire mzimu+ chifukwa Yesu anali asanalandire ulemerero wake.+