Mateyu 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Akudya chakudyacho iye ananena kuti: “Ndithu ndikukuuzani, mmodzi wa inu andipereka.”+ Maliko 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo atakhala patebulo nʼkumadya chakudya, Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani, mmodzi wa inu, amene akudya nane limodzi, andipereka.”+ Luka 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma taonani! Wondipereka ndili naye limodzi patebulo pompano.+ Yohane 6:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Yesu anawauza kuti: “Ine ndinakusankhani inu 12, si choncho?+ Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”*+
18 Ndipo atakhala patebulo nʼkumadya chakudya, Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani, mmodzi wa inu, amene akudya nane limodzi, andipereka.”+
70 Yesu anawauza kuti: “Ine ndinakusankhani inu 12, si choncho?+ Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”*+