Yohane 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndikukusiyirani mtendere ndipo ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu ngati mmene dziko limauperekera. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha.
27 Ndikukusiyirani mtendere ndipo ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu ngati mmene dziko limauperekera. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha.