Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ine ndakuuzani zimenezi kuti mukhale mu mtendere chifukwa cha ine.+ Mʼdzikomu mukumana ndi mavuto aakulu, koma limbani mtima. Ine ndaligonjetsa dziko.”+

  • Aefeso 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chifukwa iye amene anaphatikiza magulu awiri aja kukhala gulu limodzi+ nʼkugwetsa khoma lomwe linkawalekanitsa limene linali pakati pawo,+ watibweretsera mtendere.+

  • Afilipi 4:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse.+ Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipemphera kwa Mulungu, muzimuchonderera kuti azikutsogolerani pa chilichonse ndipo nthawi zonse muzimuthokoza.+ 7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene anthu sangathe kuumvetsa, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu pamene mukutsatira Khristu Yesu.

  • Akolose 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Komanso lolani kuti mtendere wa Khristu ulamulire mʼmitima yanu,+ popeza munaitanidwa ku mtendere umenewu monga ziwalo za thupi limodzi. Ndipo sonyezani kuti ndinu oyamikira.

  • 2 Atesalonika 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano Ambuye wamtendere akupatseni mtendere nthawi zonse mʼnjira iliyonse.+ Ambuye akhale nanu nonsenu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena