Yohane 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndikukusiyirani mtendere ndipo ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu ngati mmene dziko limauperekera. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha. Aefeso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa iye amene anaphatikiza magulu awiri aja kukhala gulu limodzi+ nʼkugwetsa khoma lomwe linkawalekanitsa limene linali pakati pawo,+ watibweretsera mtendere.+
27 Ndikukusiyirani mtendere ndipo ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu ngati mmene dziko limauperekera. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha.
14 Chifukwa iye amene anaphatikiza magulu awiri aja kukhala gulu limodzi+ nʼkugwetsa khoma lomwe linkawalekanitsa limene linali pakati pawo,+ watibweretsera mtendere.+