33 Ine ndakuuzani zimenezi kuti mukhale mu mtendere chifukwa cha ine.+ Mʼdzikomu mukumana ndi mavuto aakulu, koma limbani mtima. Ine ndaligonjetsa dziko.”+
5Popeza tsopano tikuonedwa kuti ndife olungama chifukwa chokhala ndi chikhulupiriro,+ tingathe kukhala pa mtendere* ndi Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+