Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 14:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Sindilankhula nanu zambiri chifukwa wolamulira wa dziko+ akubwera ndipo alibe mphamvu pa ine.+

  • Machitidwe 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mʼmalo onsewa ankalimbitsa ophunzira+ komanso kuwathandiza kuti apitirize kukhala ndi chikhulupiriro. Ankawauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi mavuto ambiri kuti tikalowe mu Ufumu wa Mulungu.”+

  • 1 Yohane 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana okondedwa, inu ndi ochokera kwa Mulungu, ndipo mwagonjetsa aneneri abodzawo.+ Zili choncho chifukwa amene ali wogwirizana ndi inu+ ndi wamkulu kuposa amene ali wogwirizana ndi dziko.+

  • 1 Yohane 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Aliyense amene ndi mwana wa Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo chikhulupiriro chathu chatithandiza kugonjetsa dziko.+

  • Chivumbulutso 3:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena