Yohane 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Si inu amene munandisankha, koma ine ndinakusankhani kuti mupitirize kubereka zipatso zochuluka, komanso kuti zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate mʼdzina langa akupatseni.+ Yohane 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsiku limenelo simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, ngati mungapemphe chilichonse kwa Atate+ mʼdzina langa adzakupatsani.+
16 Si inu amene munandisankha, koma ine ndinakusankhani kuti mupitirize kubereka zipatso zochuluka, komanso kuti zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate mʼdzina langa akupatseni.+
23 Pa tsiku limenelo simudzandifunsanso mafunso. Ndithudi ndikukuuzani, ngati mungapemphe chilichonse kwa Atate+ mʼdzina langa adzakupatsani.+