Yohane 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuyambira panopa kupita mʼtsogolo, ndizikuuziranitu zisanachitike, kuti zikadzachitika mudzakhulupirire kuti amene munkamuyembekezera uja ndi ine.+ Yohane 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ndakuuzani zisanachitike, kuti zikachitika mukhulupirire.+
19 Kuyambira panopa kupita mʼtsogolo, ndizikuuziranitu zisanachitike, kuti zikadzachitika mudzakhulupirire kuti amene munkamuyembekezera uja ndi ine.+