Yohane 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuyambira panopa kupita mʼtsogolo, ndizikuuziranitu zisanachitike, kuti zikadzachitika mudzakhulupirire kuti amene munkamuyembekezera uja ndi ine.+ Yohane 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe ndakuuzani zinthu zimenezi, kuti nthawi yoti zichitike ikadzafika, mudzakumbukire kuti ndinakuuzani.+ Zinthu zimenezi sindinakuuzeni pachiyambi chifukwa ndinali pamodzi ndi inu.
19 Kuyambira panopa kupita mʼtsogolo, ndizikuuziranitu zisanachitike, kuti zikadzachitika mudzakhulupirire kuti amene munkamuyembekezera uja ndi ine.+
4 Komabe ndakuuzani zinthu zimenezi, kuti nthawi yoti zichitike ikadzafika, mudzakumbukire kuti ndinakuuzani.+ Zinthu zimenezi sindinakuuzeni pachiyambi chifukwa ndinali pamodzi ndi inu.