Yohane 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndalankhula zinthu zimenezi kwa inu, kuti nthawi yake ikadzafika, mudzakumbukire kuti ndinakuuzani zimenezi.+ “Zinthu izi sindinakuuzeni pa chiyambi pomwe, chifukwa ndinali pamodzi ndi inu. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:4 Yesu—Ndi Njira, tsa. 278 Nsanja ya Olonda,9/1/1990, tsa. 8
4 Ine ndalankhula zinthu zimenezi kwa inu, kuti nthawi yake ikadzafika, mudzakumbukire kuti ndinakuuzani zimenezi.+ “Zinthu izi sindinakuuzeni pa chiyambi pomwe, chifukwa ndinali pamodzi ndi inu.