Yohane 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake. Popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera mʼdziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+ Yakobo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Achigololo inu,* kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko nʼkudziika pa udani ndi Mulungu? Choncho aliyense amene akufuna kukhala bwenzi la dziko akudzipangitsa kuti akhale mdani wa Mulungu.+
19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake. Popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera mʼdziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+
4 Achigololo inu,* kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko nʼkudziika pa udani ndi Mulungu? Choncho aliyense amene akufuna kukhala bwenzi la dziko akudzipangitsa kuti akhale mdani wa Mulungu.+