Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya, anapita kwa Mfumu Yehosafati ndipo anamufunsa kuti: “Kodi muyenera kuthandiza anthu oipa,+ ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani.

  • Yohane 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake. Popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera mʼdziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+

  • Yohane 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo ndawapatsa mawu anu, koma dziko likudana nawo chifukwa sali mbali ya dziko,+ mofanana ndi ine amene sindili mbali ya dziko.

  • Yohane 18:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Yesu anayankha kuti:+ “Ufumu wanga si wamʼdzikoli.+ Ufumu wanga ukanakhala wamʼdzikoli, atumiki anga akanamenya nkhondo kuti ndisaperekedwe kwa Ayuda.+ Koma Ufumu wanga si wochokera mʼdzikoli.”

  • 1 Yohane 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Musamakonde dziko kapena zinthu zamʼdziko.+ Ngati wina akukonda dziko, ndiye kuti sakonda Atate.+

  • 1 Yohane 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tikudziwa kuti ndife anthu a Mulungu, koma dziko lonse lili mʼmanja mwa woipayo.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena